-
Yeremiya 25:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Tamverani! Ngati ndikuyamba kubweretsa tsoka pa mzinda umene ukutchedwa ndi dzina langa,+ ndiye kodi inuyo simukuyenera kulandira chilango?”’+
‘Simulephera kulangidwa chifukwa ndikuitana lupanga kuti liwononge anthu onse amene akukhala padziko lapansi,’ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-