Yeremiya 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ‘Phokoso lidzamveka kumalekezero a dziko lapansi,Chifukwa Yehova akufuna kuimba mlandu mitundu ya anthu. Iye adzapereka yekha chiweruzo kwa anthu onse.+ Ndipo anthu oipa adzawapha ndi lupanga,’ akutero Yehova. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:31 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 22
31 ‘Phokoso lidzamveka kumalekezero a dziko lapansi,Chifukwa Yehova akufuna kuimba mlandu mitundu ya anthu. Iye adzapereka yekha chiweruzo kwa anthu onse.+ Ndipo anthu oipa adzawapha ndi lupanga,’ akutero Yehova.