-
Yeremiya 25:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Pa tsiku limenelo anthu amene adzaphedwe ndi Yehova adzachokera kumalekezero a dziko lapansi kukafika kumalekezero ena a dziko lapansi. Maliro awo sadzaliridwa, sadzawasonkhanitsa pamodzi kapena kuwaika mʼmanda. Iwo adzakhala ngati manyowa panthaka.’
-