-
Yeremiya 25:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Fuulani ndipo lirani abusa inu!
Gubuduzikani inu anthu olemekezeka pa gulu la nkhosa,
Chifukwa nthawi yoti muphedwe komanso yoti mubalalitsidwe yafika,
Ndipo mudzagwa ndi kuphwanyika ngati chiwiya chamtengo wapatali.
-