Yeremiya 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwina adzamvera ndipo aliyense wa iwo adzabwerera kuchoka panjira yake yoipa. Ndipo ndidzasintha maganizo anga okhudza tsoka limene ndikufuna kuwagwetsera chifukwa cha zochita zawo zoipa.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:3 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Yeremiya, tsa. 151
3 Mwina adzamvera ndipo aliyense wa iwo adzabwerera kuchoka panjira yake yoipa. Ndipo ndidzasintha maganizo anga okhudza tsoka limene ndikufuna kuwagwetsera chifukwa cha zochita zawo zoipa.+