-
Yeremiya 26:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Yeremiya atamaliza kulankhula mawu onse amene Yehova anamulamula kuti akauze anthu onse, nthawi yomweyo ansembe, aneneri ndi anthu onse anamugwira nʼkunena kuti: “Ukuyenera kufa basi.
-