-
Yeremiya 26:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Nʼchifukwa chiyani wanenera mʼdzina la Yehova kuti, ‘Nyumba iyi idzakhala ngati Silo ndipo mzinda uwu udzawonongedwa moti simudzapezeka aliyense wokhalamoʼ?” Ndiyeno anthu onse anabwera mʼnyumba ya Yehova nʼkuzungulira Yeremiya.
-