Yeremiya 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akalonga a Yuda atamva mawu amenewa, anachoka kunyumba ya mfumu nʼkupita kunyumba ya Yehova ndipo anakakhala pakhomo lapageti latsopano la nyumba ya Yehova.+
10 Akalonga a Yuda atamva mawu amenewa, anachoka kunyumba ya mfumu nʼkupita kunyumba ya Yehova ndipo anakakhala pakhomo lapageti latsopano la nyumba ya Yehova.+