Yeremiya 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ansembe ndi aneneri anauza akalongawo ndi anthu onse kuti: “Munthuyu akuyenera kuphedwa+ chifukwa wanenera zoti mzindawu udzakumana ndi tsoka monga mmene mwamvera ndi makutu anu.”+
11 Ansembe ndi aneneri anauza akalongawo ndi anthu onse kuti: “Munthuyu akuyenera kuphedwa+ chifukwa wanenera zoti mzindawu udzakumana ndi tsoka monga mmene mwamvera ndi makutu anu.”+