Yeremiya 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho panopa sinthani njira zanu komanso zochita zanu ndipo muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu. Mukatero, Yehova adzasintha maganizo ake okhudza tsoka limene wanena kuti akugwetserani.+
13 Choncho panopa sinthani njira zanu komanso zochita zanu ndipo muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu. Mukatero, Yehova adzasintha maganizo ake okhudza tsoka limene wanena kuti akugwetserani.+