19 Kodi Hezekiya mfumu ya Yuda ndi anthu onse a mu Yuda anamupha? Kodi iye sanaope Yehova komanso kupempha Yehova kuti amukomere mtima? Atatero, kodi Yehova sanasinthe maganizo ake pa tsoka limene ananena kuti adzawabweretsera?+ Pamenepatu ife tikudziitanira tsoka lalikulu.