Yeremiya 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Ine ndi amene ndinapanga dziko lapansi, anthu ndi nyama zapadziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zanga zazikulu ndiponso dzanja langa lotambasula. Ndipo dziko lapansili ndalipereka kwa amene ndikufuna.*+
5 ‘Ine ndi amene ndinapanga dziko lapansi, anthu ndi nyama zapadziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zanga zazikulu ndiponso dzanja langa lotambasula. Ndipo dziko lapansili ndalipereka kwa amene ndikufuna.*+