Yeremiya 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma mtundu wa anthu umene udzaike khosi lake mʼgoli la mfumu ya Babulo nʼkuitumikira, ndidzaulola kuti ukhalebe* mʼdziko lawo ndipo udzalima minda nʼkumakhala mʼdzikolo,’ akutero Yehova.”’”
11 Koma mtundu wa anthu umene udzaike khosi lake mʼgoli la mfumu ya Babulo nʼkuitumikira, ndidzaulola kuti ukhalebe* mʼdziko lawo ndipo udzalima minda nʼkumakhala mʼdzikolo,’ akutero Yehova.”’”