Yeremiya 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi iweyo ndi anthu ako muferenji ndi lupanga,+ njala+ ndi mliri+ ngati mmene Yehova wanenera kuti ndi zimene zidzachitikire mtundu umene sudzatumikira mfumu ya Babulo?
13 Kodi iweyo ndi anthu ako muferenji ndi lupanga,+ njala+ ndi mliri+ ngati mmene Yehova wanenera kuti ndi zimene zidzachitikire mtundu umene sudzatumikira mfumu ya Babulo?