Yeremiya 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 zimene Nebukadinezara mfumu ya Babulo sanatenge pamene ankatenga Yekoniya mwana wa Yehoyakimu, mfumu ya Yuda, pamodzi ndi olemekezeka onse a Yuda ndi Yerusalemu, kupita nawo ku ukapolo ku Babulo kuchokera ku Yerusalemu.+
20 zimene Nebukadinezara mfumu ya Babulo sanatenge pamene ankatenga Yekoniya mwana wa Yehoyakimu, mfumu ya Yuda, pamodzi ndi olemekezeka onse a Yuda ndi Yerusalemu, kupita nawo ku ukapolo ku Babulo kuchokera ku Yerusalemu.+