-
Yeremiya 27:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena zokhudza ziwiya zimene zinatsala mʼnyumba ya Yehova, mʼnyumba ya mfumu ya Yuda ndi zimene zinatsala ku Yerusalemu kuti:
-