Yeremiya 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ‘“Ziwiya zimenezi zidzapita ku Babulo+ ndipo zidzakhala kumeneko mpaka tsiku limene ndidzazikumbukire,” akutero Yehova. “Ndipo ndidzazitenga nʼkuzibwezeretsa pamalo ano.”’”+
22 ‘“Ziwiya zimenezi zidzapita ku Babulo+ ndipo zidzakhala kumeneko mpaka tsiku limene ndidzazikumbukire,” akutero Yehova. “Ndipo ndidzazitenga nʼkuzibwezeretsa pamalo ano.”’”+