Yeremiya 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zaka ziwiri zisanathe, ndibwezeretsa pamalo ano ziwiya zonse zamʼnyumba ya Yehova zimene Nebukadinezara mfumu ya Babulo anatenga kuno nʼkupita nazo ku Babulo.’”+
3 Zaka ziwiri zisanathe, ndibwezeretsa pamalo ano ziwiya zonse zamʼnyumba ya Yehova zimene Nebukadinezara mfumu ya Babulo anatenga kuno nʼkupita nazo ku Babulo.’”+