Yeremiya 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hananiya atamva zimenezo anatenga goli limene linali mʼkhosi mwa mneneri Yeremiya nʼkulithyola.+