-
Yeremiya 29:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Awa ndi mawu amʼkalata imene mneneri Yeremiya anatumiza kuchokera ku Yerusalemu kupita kwa akuluakulu onse amene anali mʼgulu la anthu amene anali ku ukapolo, kwa ansembe, kwa aneneri ndi kwa anthu onse amene Nebukadinezara anawatenga ku Yerusalemu nʼkupita nawo ku ukapolo ku Babulo.
-