Yeremiya 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Analemba kalata imeneyi pambuyo poti Mfumu Yekoniya,+ mayi a mfumu,+ nduna zapanyumba ya mfumu, akalonga a Yuda ndi Yerusalemu, amisiri komanso anthu osula zitsulo* achoka ku Yerusalemu.+
2 Analemba kalata imeneyi pambuyo poti Mfumu Yekoniya,+ mayi a mfumu,+ nduna zapanyumba ya mfumu, akalonga a Yuda ndi Yerusalemu, amisiri komanso anthu osula zitsulo* achoka ku Yerusalemu.+