Yeremiya 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo mzinda umene ndakupititsani kuti mukakhale akapolo, muziufunira mtendere. Muziupempherera kwa Yehova chifukwa mzindawo ukakhala pa mtendere inunso mudzakhala pa mtendere.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:7 Nsanja ya Olonda,5/1/1996, tsa. 11
7 Ndipo mzinda umene ndakupititsani kuti mukakhale akapolo, muziufunira mtendere. Muziupempherera kwa Yehova chifukwa mzindawo ukakhala pa mtendere inunso mudzakhala pa mtendere.+