Yeremiya 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Musalole kuti aneneri anu komanso anthu ochita zamaula amene ali pakati panu akupusitseni+ ndipo musamvere maloto amene alota. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:8 Nsanja ya Olonda,10/1/1996, tsa. 5
8 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Musalole kuti aneneri anu komanso anthu ochita zamaula amene ali pakati panu akupusitseni+ ndipo musamvere maloto amene alota.