Yeremiya 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa ‘akulosera zabodza kwa inu mʼdzina langa. Ine sindinawatume,’+ akutero Yehova.”’”