Yeremiya 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Izi ndi zimene Yehova akunena kwa mfumu imene ikukhala pampando wachifumu wa Davide+ ndiponso kwa anthu onse amene akukhala mumzinda wa Yerusalemu, abale anu amene sanapite nanu ku ukapolo,
16 Izi ndi zimene Yehova akunena kwa mfumu imene ikukhala pampando wachifumu wa Davide+ ndiponso kwa anthu onse amene akukhala mumzinda wa Yerusalemu, abale anu amene sanapite nanu ku ukapolo,