Yeremiya 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ine ndikuwatumizira lupanga, njala ndi mliri*+ ndipo ndidzawachititsa kuti akhale ngati nkhuyu zowola* zimene ndi zoipa kwambiri moti munthu sangadye.”’+
17 ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ine ndikuwatumizira lupanga, njala ndi mliri*+ ndipo ndidzawachititsa kuti akhale ngati nkhuyu zowola* zimene ndi zoipa kwambiri moti munthu sangadye.”’+