-
Yeremiya 29:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndipo zimene zidzawachitikire zidzakhala temberero limene anthu amene anatengedwa ku Yuda kupita ku ukapolo ku Babulo azidzanena kuti: “Yehova akuchititse kuti ukhale ngati Zedekiya ndi Ahabu amene mfumu ya Babulo inawawotcha pamoto!”
-