Yeremiya 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa anachita zinthu zochititsa manyazi mu Isiraeli.+ Ankachita chigololo ndi akazi a anzawo komanso akulankhula zabodza mʼdzina langa zimene ine sindinawalamule.+ “Ine ndikuzidziwa zimenezi ndipo ndine mboni,”+ akutero Yehova.’”
23 Chifukwa anachita zinthu zochititsa manyazi mu Isiraeli.+ Ankachita chigololo ndi akazi a anzawo komanso akulankhula zabodza mʼdzina langa zimene ine sindinawalamule.+ “Ine ndikuzidziwa zimenezi ndipo ndine mboni,”+ akutero Yehova.’”