Yeremiya 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Chifukwa chakuti watumiza makalata mʼdzina lako kwa anthu onse amene ali ku Yerusalemu, kwa Zefaniya+ mwana wa Maaseya, amene ndi wansembe ndi kwa ansembe onse, onena kuti,
25 ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Chifukwa chakuti watumiza makalata mʼdzina lako kwa anthu onse amene ali ku Yerusalemu, kwa Zefaniya+ mwana wa Maaseya, amene ndi wansembe ndi kwa ansembe onse, onena kuti,