Yeremiya 29:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye watitumizira kalata kuno ku Babulo yonena kuti: “Mukhala akapolo kwa nthawi yaitali. Mangani nyumba nʼkumakhalamo. Limani minda nʼkumadya zipatso zake,+ . . .”’”’”
28 Iye watitumizira kalata kuno ku Babulo yonena kuti: “Mukhala akapolo kwa nthawi yaitali. Mangani nyumba nʼkumakhalamo. Limani minda nʼkumadya zipatso zake,+ . . .”’”’”