31 “Anthu onse amene ali ku ukapolo uwatumizire uthenga wakuti, ‘Ponena za Semaya wa ku Nehelamu, Yehova wanena kuti: “Popeza Semaya analosera kwa inu, ngakhale kuti ine sindinamutume ndipo anayesetsa kukuchititsani kuti mukhulupirire zinthu zabodza,+