Yeremiya 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tafunsani, kodi mwamuna angabereke mwana? Nanga nʼchifukwa chiyani ndikuona mwamuna aliyense wamphamvu atagwira manja pamimba* pakeNgati mkazi amene akubereka?+ Nʼchifukwa chiyani aliyense nkhope yake yafooka?
6 Tafunsani, kodi mwamuna angabereke mwana? Nanga nʼchifukwa chiyani ndikuona mwamuna aliyense wamphamvu atagwira manja pamimba* pakeNgati mkazi amene akubereka?+ Nʼchifukwa chiyani aliyense nkhope yake yafooka?