Yeremiya 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mayo ine! Chifukwa tsiku limenelo lidzakhala lochititsa mantha.*+ Ndipo palibe lofanana nalo.Tsiku limenelo lidzakhala lamavuto kwa Yakobo. Koma adzapulumutsidwa mʼmavuto amenewa.
7 Mayo ine! Chifukwa tsiku limenelo lidzakhala lochititsa mantha.*+ Ndipo palibe lofanana nalo.Tsiku limenelo lidzakhala lamavuto kwa Yakobo. Koma adzapulumutsidwa mʼmavuto amenewa.