-
Yeremiya 30:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Pa tsiku limenelo ndidzathyola goli limene lili mʼkhosi lanu. Ndidzadula pakati zingwe zimene akumangani nazo, moti anthu achilendo sadzachititsanso kuti Yakobo akhale kapolo wawo,” akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-