-
Yeremiya 30:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Palibe woti akuchonderere pa mlandu wako.
Palibe njira iliyonse yochiritsira bala lako.
Ndipo palibe mankhwala amene angakuchiritse.
-