Yeremiya 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Onse amene ankakukonda kwambiri akuiwala.+ Iwo sakukufunafunanso. Ndakumenya ngati mmene angakumenyere mdani,+Ndipo ndakulanga ngati mmene angakulangire munthu wankhanza,Chifukwa cha kulakwa kwako kwakukulu ndi kuchuluka kwa machimo ako.+
14 Onse amene ankakukonda kwambiri akuiwala.+ Iwo sakukufunafunanso. Ndakumenya ngati mmene angakumenyere mdani,+Ndipo ndakulanga ngati mmene angakulangire munthu wankhanza,Chifukwa cha kulakwa kwako kwakukulu ndi kuchuluka kwa machimo ako.+