Yeremiya 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi pali chifukwa choti udandaulire ndi chilango chimene wapatsidwa? Ululu wako ndi wosachiritsika. Chifukwa cha kulakwa kwako kwakukulu ndi kuchuluka kwa machimo ako,+Ine ndakuchitira zimenezi.
15 Kodi pali chifukwa choti udandaulire ndi chilango chimene wapatsidwa? Ululu wako ndi wosachiritsika. Chifukwa cha kulakwa kwako kwakukulu ndi kuchuluka kwa machimo ako,+Ine ndakuchitira zimenezi.