Yeremiya 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzakuchititsa kuti ukhalenso wathanzi ndipo ndidzapoletsa mabala ako,”+ akutero Yehova.“Ngakhale kuti anakana kukulandira ndipo anakutchula kuti: ‘Ziyoni amene palibe amene akumufunafuna.’”+
17 Ndidzakuchititsa kuti ukhalenso wathanzi ndipo ndidzapoletsa mabala ako,”+ akutero Yehova.“Ngakhale kuti anakana kukulandira ndipo anakutchula kuti: ‘Ziyoni amene palibe amene akumufunafuna.’”+