Yeremiya 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kwa iwo kudzamveka mawu oyamikira ndi phokoso la kuseka kwa anthu.+ Ndidzawachulukitsa moti sadzakhala ochepa.+Ndidzawachititsa kuti akhale ambiri,*Ndipo sadzakhala anthu ochepa.+
19 Kwa iwo kudzamveka mawu oyamikira ndi phokoso la kuseka kwa anthu.+ Ndidzawachulukitsa moti sadzakhala ochepa.+Ndidzawachititsa kuti akhale ambiri,*Ndipo sadzakhala anthu ochepa.+