Yeremiya 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ana ake aamuna zinthu zidzawayendera bwino ngati mmene zinalili poyamba,Ndipo ndidzawapangitsa kuti akhale anthu amphamvu pamaso panga.+ Ndidzalanga anthu onse amene amamupondereza.+
20 Ana ake aamuna zinthu zidzawayendera bwino ngati mmene zinalili poyamba,Ndipo ndidzawapangitsa kuti akhale anthu amphamvu pamaso panga.+ Ndidzalanga anthu onse amene amamupondereza.+