Yeremiya 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Taonani! Mkwiyo wa Yehova udzawomba ngati mphepo yamkuntho,+Udzawomba ngati kamvulumvulu wamphamvu pamitu ya anthu oipa.
23 Taonani! Mkwiyo wa Yehova udzawomba ngati mphepo yamkuntho,+Udzawomba ngati kamvulumvulu wamphamvu pamitu ya anthu oipa.