Yeremiya 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli ndipo iwo adzakhala anthu anga,” akutero Yehova.+
31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli ndipo iwo adzakhala anthu anga,” akutero Yehova.+