Yeremiya 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Pa nthawi imeneyo, anamwali,Anyamata ndiponso amuna achikulire, adzavina pamodzi mosangalala.+ Kulira kwawo ndidzakusandutsa chisangalalo.+ Ndidzawatonthoza ndipo ndidzachititsa kuti akhale osangalala mʼmalo mokhala achisoni.+
13 “Pa nthawi imeneyo, anamwali,Anyamata ndiponso amuna achikulire, adzavina pamodzi mosangalala.+ Kulira kwawo ndidzakusandutsa chisangalalo.+ Ndidzawatonthoza ndipo ndidzachititsa kuti akhale osangalala mʼmalo mokhala achisoni.+