Yeremiya 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Taonani! Masiku akubwera, pamene ndidzachititsa kuti nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda ikhalenso ndi anthu ochuluka komanso ziweto zambiri,” akutero Yehova.+
27 “Taonani! Masiku akubwera, pamene ndidzachititsa kuti nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda ikhalenso ndi anthu ochuluka komanso ziweto zambiri,” akutero Yehova.+