32 “Koma silidzakhala pangano lofanana ndi limene ndinachita ndi makolo awo, pa tsiku limene ndinagwira dzanja lawo kuti ndiwatulutse mʼdziko la Iguputo.+ ‘Pangano langa limenelo analiphwanya+ ngakhale kuti ine ndinali mbuye wawo weniweni,’ akutero Yehova.”