Yeremiya 31:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “‘Ngati malamulo amenewa angalephere kugwira ntchito yake,Ndiye kutinso mbadwa za Isiraeli zingasiye kukhala mtundu, umene umakhala pamaso panga nthawi zonse,’ akutero Yehova.”+
36 “‘Ngati malamulo amenewa angalephere kugwira ntchito yake,Ndiye kutinso mbadwa za Isiraeli zingasiye kukhala mtundu, umene umakhala pamaso panga nthawi zonse,’ akutero Yehova.”+