Yeremiya 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mfumu Zedekiya ya Yuda inamutsekera+ kumeneko nʼkunena kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukulosera zimenezi? Ukunena kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Mzindawu ndidzaupereka mʼmanja mwa mfumu ya Babulo ndipo idzaulanda,+
3 Mfumu Zedekiya ya Yuda inamutsekera+ kumeneko nʼkunena kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukulosera zimenezi? Ukunena kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Mzindawu ndidzaupereka mʼmanja mwa mfumu ya Babulo ndipo idzaulanda,+