Yeremiya 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zanu zazikulu+ ndi dzanja lanu lotambasula. Palibe chimene chingakuvuteni.
17 “Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Inuyo ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zanu zazikulu+ ndi dzanja lanu lotambasula. Palibe chimene chingakuvuteni.