Yeremiya 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu munachita zizindikiro ndi zodabwitsa mʼdziko la Iguputo zimene zikudziwikabe mpaka lero. Ndipo zimenezo zinachititsa kuti dzina lanu lidziwike mu Isiraeli komanso pakati pa anthu onse+ ngati mmene likudziwikira lero.
20 Inu munachita zizindikiro ndi zodabwitsa mʼdziko la Iguputo zimene zikudziwikabe mpaka lero. Ndipo zimenezo zinachititsa kuti dzina lanu lidziwike mu Isiraeli komanso pakati pa anthu onse+ ngati mmene likudziwikira lero.