Yeremiya 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ‘Aisiraeli ndi Ayuda akhala akuchita zoipa zokhazokha pamaso panga kuyambira ali ana.+ Aisiraeli akhala akundikhumudwitsa ndi ntchito za manja awo,’ akutero Yehova.
30 ‘Aisiraeli ndi Ayuda akhala akuchita zoipa zokhazokha pamaso panga kuyambira ali ana.+ Aisiraeli akhala akundikhumudwitsa ndi ntchito za manja awo,’ akutero Yehova.